Opuma pa ntchito ya m’boma akuvutika chifukwa sanalandilebe ndalama zawo za pensoni
Mayi Nellie Mkhumba ndi Tcheya ndi owulutsa nkhani, bambo Ben Mitochi * Boma likalephera kupeleka ndalama yo pofika kumapeto a mwezi wa August 2025 azatsatira njira zina monga kupita ku khothi * Kapenanso kuchita zionetselo za bata ku ma ofesi Tresuary ku Capital Hill ku Lilongwe kuyambira lachiwiri pa September 2 osachoka mpaka onse atalipidwa Wolemba Duncan Mlanjira Omwe ankagwira ntchito m’boma (civil servants) amene anapuma ntchito (Penshoniya) kuyambira 2022 mpaka 2025, akuvutika kwambiri chifukwa sanalandilebe ndalama zawo za…