Abuse of Sex Workers Rife; Police Officer Cut Off Sex worker’s Finger

A 29-year-old woman, Chimwemwe Chariwa, has raised claims that Kasungu Police officers abused her for allegedly selling stolen property on Wednesday last week. According to Chariwa who plies her trade as a sex worker, one police officer asked her to help them apprehend a suspected criminal who has been eluding the police but heard that he often goes to the rest house where Chariwa and other sex workers put up. “Fortunately, the suspected criminal was a person who came…

Read More

Villagers in Shock As 89 Year Old Man Commits Suicide

89 year old man identified as Stenala Matiya from Mpanje village, Traditional Authority Chiwere in Dowa district was on Friday, February 23, 2018   committed suicide at Mpingu Trading Centre in Lilongwe. According to Lilongwe Police Spokesperson Kingsly Dandaula, on February 21,2018 head teacher for Lowe LEA School at Mpingu reported the matter to Lilongwe police that his father the deceased hanged himself in his bedroom. He said that on the said date the reporter and other family members were…

Read More

Malawian Man Jailed 11 Years For Defiling Step Daughter

Dedza First Grade Magistrate Court has sentenced a 25 year old Man identified as Kasito Yasini for defiling his 11 year old step daughter in order to become rich. Police Prosecutor Sub Inspector Wedson Nyondo told the court that Yasini got charms from a certain herbalist to get rich and as a ritual, he was supposed to sleep with an under aged girl and on 2nd February, 2018 he forced his stepdaughter into his bedroom where he had sex…

Read More

Gule Wamkulu Arrested for Wounding 3-Year-Old Girl

Nkhotakota Police Station is keeping in custody a Gule wamkulu Kamano dancer for unlawfully injuring a three year old girl during his performance. The Station’s Public Relations Officer (PRO), Williams Kaponda identified the Gule wamkulu dancer as 27 year old Pilirani Ching’oma of Khufu Village, Senior Chief Malengachanzi in the district. He said that the incident happened on January 3,2017 at Kapenda Village, Senior Chief Malengachanzi where gule wamkulu organised an event to entertain people from surrounding villages. “As…

Read More

Teacher with 7 Classes: Ministry of Education Deploys Teachers to School

Ministry of Education Science and Technology through the Blantyre District Education Manager’s office (DEM) on Friday deployed two qualified teachers to Chiguma primary school which, for the past two years, was being handled by a single but volunteer teacher – Mark Kamphira. The story of Kamphira and Chiguma School was first carried by Malawi News Agency (MANA) when the school was being handed over to government by Majete wildlife and parks in November last year. Chiguma primary school currently…

Read More

Adabwitsa Anthu atavina mwa kaso ndi Kabuduka wa Mkati Yekha

Pamene anthu ali kalikiliki m’madera osiyanasiyana a dziko lino kukonzekera chisangalalo cha Khisimesi cha chaka chino nalonso tsamba la zikuchitika pa Maravi Express likunka limwaza maso ake ndi cholinga chofuna kukudziwitsani nkhani zochitisa chidwi zomwe zayamba kale kuchitika padakali pano. Anthu ambiri omwe amachita bizinezi zosiyana siyana pa msika wa Bvumbwe nawonso anayima mitu pamene bambo wina anavina ndi msungwana wina ndi kugwetserana pansi yemwe anavula zovala zake nkusala ndi kabudula wa mkati yekha kwinaku ati kamba ka nyimbo…

Read More

Ayaluka Atapezeleredwa Akuchita za Dama ndi Mwana Omupeza

Zina ukamva akulu sadalakwitse ponena kuti kamba anga mwala. Mkulu wina yemwe akuti wakhala akunka alalikira malo osiyana-siyana mtauni ya Limbe pomadzitcha kuti ndi mneneli akuti masiku apitawa wayaluka pamene anamupezelera akuchita za dama ndi mwana wake omupeza ku bafa. Izitu zachitika ku Nthandizi mtaunishipi ya Bangwe. Malinga ndi kunena kwa bambo omwe anangozitchula kuti ndi a Macheso omwe amakhala pafupi ndi nyumbayo, iye wakhala akukayikitsa anthu za mayendedwe ake akamachoka pakhomo kupita mtauni ya Limbe kamba koti masiku…

Read More

Ayenda ndi Kabudula Wamkati Yekha Kamba Kolephera Kumaliza Ndime

Mkulu wina anawona ngati za kutulo masiku apitawa pamene anavulidwa zovala zonse nkusala ndi kabudula wamkati yekha pa malo ena omwela mowa ndi msungwana wina yemwe anamulemba ganyu yoti amuthandize kulima munda wake omwe uli pa mudzi wa William mdera la mfumu yaikulu Bvumbwe m’boma la Thyolo. Mayi Naomi Benadi omwe anawona izi zikuchitika maso ndi maso anafotokoza kuti mkuluyo wakhala akuchita khalidwe limeneli kwa nthawi yaitali lomanka alandila ndalama zonse akafunsa ganyu koma akangoyamba ndime samaliza popeza amathawa…

Read More

Alira Chokweza pa Msika Kamba Kopheledwa Njoka

Mkulu wina yemwe amachita geni ya wokala pa msika wa Makhetha ku Machinjiri munzinda wotchuka kunkhani ya zamalonda wa Blantyre akuti masiku apitawa anadabwitsa anthu pamene analira chokweza atazindikira kuti anthu ena pamsikawo apha njoka yomwe imadutsa kuseli kwa mawokala ena. Malinga ndi kunena kwa bambo Mikeyasi omwe amachita geni ya nsomba za manyalira pa msikawo, nkhaniyi akuti inachitika masiku apitawa pamene anthu mumsikawo amadabwa ndi m’mene geni ya mkuluyo imapitira patsogolo kamba koti anayamba ndi kakhobili kochepa zaka…

Read More

Athetsa Banja Atamupezelera Akuchita za Dama Dzuwa Likuswa Mtengo

Mkulu wina kwa Bvumbwe mboma la Thyolo akuti akuyenda zolizoli ngati nkhuku ya Chitopa kamba ka manyazi atamupezelera akuchita za dama ndi msungwana woyendayenda kuseli kwa malo ena omwera chakumwa chaukali. Bambo Misheck omwe anawona izi zikuchitika maso ndi maso masiku apitawa anafotokozera Maravi Express kuti mkuluyo wakhala akuchita mchitidwewu mozembera mkazi wake yemwe anamubelekera ana atatu. Ndiye paja akulu amati ukatambatamba udziyamba kaye wayang’ana kunyanja kamba koti kunja kungakuchere, iye anawona ngati kutulo pamene anthu ena omwe ankamwa…

Read More